Bản dịch ý nghĩa nội dung Qur'an - 齐切瓦语翻译 - 哈利德·伊布拉欣·白塔俩

external-link copy
33 : 12

قَالَ رَبِّ ٱلسِّجۡنُ أَحَبُّ إِلَيَّ مِمَّا يَدۡعُونَنِيٓ إِلَيۡهِۖ وَإِلَّا تَصۡرِفۡ عَنِّي كَيۡدَهُنَّ أَصۡبُ إِلَيۡهِنَّ وَأَكُن مِّنَ ٱلۡجَٰهِلِينَ

(Yûsuf) adati: “E Mbuye wanga! Ndende ndi yabwino kwa ine kuposa izi akundiitanira. Ngati simundichotsera ndale zawo ndiye kuti ndiwacheukira ndikukhala mmodzi mwa mbuli.”[232] info

[232] Akazi aja atamuona Yûsuf tsiku limenelo nawonso anadzazidwa ndi chikondi chachikulu nayamba kumtumizira mithenga ndi makalata. Ndipo Yûsuf adaganiza kuti ndibwino angopita kundende poopa kuti akaziwo angamulakwitse.

التفاسير: