Përkthimi i kuptimeve të Kuranit Fisnik - Përkthimi çiçevë - Khalid Ibrahim Betiala

external-link copy
48 : 7

وَنَادَىٰٓ أَصۡحَٰبُ ٱلۡأَعۡرَافِ رِجَالٗا يَعۡرِفُونَهُم بِسِيمَىٰهُمۡ قَالُواْ مَآ أَغۡنَىٰ عَنكُمۡ جَمۡعُكُمۡ وَمَا كُنتُمۡ تَسۡتَكۡبِرُونَ

Ndipo anthu aja apachikweza adzawaitana anthu (a ku Moto), adzawadziwa ndi zizindikiro zawo, nati: “Sikudakuthandizeni kuchuluka kwanu kuja, ngakhale zija mudali kudzitama nazo.” info
التفاسير: