Vertaling van de betekenissen Edele Qur'an - Chichewa-vertaling - Khalid Ibrahim Beitala

external-link copy
65 : 27

قُل لَّا يَعۡلَمُ مَن فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ ٱلۡغَيۡبَ إِلَّا ٱللَّهُۚ وَمَا يَشۡعُرُونَ أَيَّانَ يُبۡعَثُونَ

Nena: “Palibe amene alipo kumwamba ndi pansi akudziwa zam’seri (zomwe zisanadze) kupatula Allah basi. Ndipo (amene akuwapembedza) sadziwa kuti ndiliti adzaukitsidwa ku imfa.” info
التفاسير: