Vertaling van de betekenissen Edele Qur'an - Chichewa-vertaling - Khalid Ibrahim Beitala

external-link copy
64 : 27

أَمَّن يَبۡدَؤُاْ ٱلۡخَلۡقَ ثُمَّ يُعِيدُهُۥ وَمَن يَرۡزُقُكُم مِّنَ ٱلسَّمَآءِ وَٱلۡأَرۡضِۗ أَءِلَٰهٞ مَّعَ ٱللَّهِۚ قُلۡ هَاتُواْ بُرۡهَٰنَكُمۡ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ

Kapena (wabwino) ndiamene adayambitsa zolengedwa, (ndipo) kenako adzazibweza, kapenanso amene amakupatsani rizq (chakudya) kuchokera kumwamba ndi m’nthaka? Kodi pamodzi ndi Allah pali mulungu winanso? Nena: “Bweretsani umboni wanu ngati mukunena zoona (wotsimikizira kuti Allah ali ndi mnzake).” info
التفاسير: