Fassarar Ma'anonin Alqura'ni - Fassara da harshan Shishiyo - Khalid Ibrahim Bitala

external-link copy
14 : 10

ثُمَّ جَعَلۡنَٰكُمۡ خَلَٰٓئِفَ فِي ٱلۡأَرۡضِ مِنۢ بَعۡدِهِمۡ لِنَنظُرَ كَيۡفَ تَعۡمَلُونَ

Kenako takupangani inu (Asilamu) kukhala olowa m’malo mwawo pa dziko pambuyo pawo kuti tione mmene mungachitire (zabwino kapena zoipa). info
التفاسير: