ترجمة معاني القرآن الكريم - الترجمة الشيشيوا - خالد إبراهيم بتيالا

external-link copy
76 : 6

فَلَمَّا جَنَّ عَلَيۡهِ ٱلَّيۡلُ رَءَا كَوۡكَبٗاۖ قَالَ هَٰذَا رَبِّيۖ فَلَمَّآ أَفَلَ قَالَ لَآ أُحِبُّ ٱلۡأٓفِلِينَ

Ndipo pamene kunam’dera adaona nyenyezi. Adati (mwadaladala kuti abutse nzeru za opembedza mafano): “(Nyenyezi) iyi ndiye mbuye wanga.” Pamene idalowa, adati: “Sindikonda (milungu) yomalowa, (yomasowa, yakutha).” info
التفاسير: