Kur'an-ı Kerim meal tercümesi - Çevaca Tercüme - Halid İbrahim Pitala

external-link copy
22 : 81

وَمَا صَاحِبُكُم بِمَجۡنُونٖ

Ndipo m’bale wanuyu siwamisala ayi.[396] info

[396] (Ndime 22-25) Anthu okanira pamene adasowa chonena kwa mneneri (s.a.w) adali kunena nkhani zabodza kuti Mtumiki (s.a.w) wapenga ndikuti zomwe akuyankhula sadapatsidwe ndi Jibril.

التفاسير: