Kur'an-ı Kerim meal tercümesi - Çevaca Tercüme - Halid İbrahim Pitala

external-link copy
159 : 6

إِنَّ ٱلَّذِينَ فَرَّقُواْ دِينَهُمۡ وَكَانُواْ شِيَعٗا لَّسۡتَ مِنۡهُمۡ فِي شَيۡءٍۚ إِنَّمَآ أَمۡرُهُمۡ إِلَى ٱللَّهِ ثُمَّ يُنَبِّئُهُم بِمَا كَانُواْ يَفۡعَلُونَ

Ndithudi, anthu amene achigawa Chipembedzo chawo, nakhala Mipingomipingo, iwe Siuli nawo pachilichonse. Ndithu zotsatira zawo zili kwa Allah, (ndi yemwe adzawalanga. Ndipo panthawi yowalanga) adzawauza zomwe adali kuchita. info
التفاسير: