Tradução dos significados do Nobre Qur’an. - Tradução para a língua chachio - Khalid Ibrahim Batyala

external-link copy
34 : 34

وَمَآ أَرۡسَلۡنَا فِي قَرۡيَةٖ مِّن نَّذِيرٍ إِلَّا قَالَ مُتۡرَفُوهَآ إِنَّا بِمَآ أُرۡسِلۡتُم بِهِۦ كَٰفِرُونَ

Palibe pamene tidatuma mchenjezi m’mudzi uliwonse koma opeza bwino a m’mudzimo ankanena: “Ndithu ife tikuzikana zimene mwatumidwa nazozi.” info
التفاسير: