Kilniojo Korano reikšmių vertimas - Vertimas į čevų k. - Khalid Ibrahim Bitala

external-link copy
159 : 7

وَمِن قَوۡمِ مُوسَىٰٓ أُمَّةٞ يَهۡدُونَ بِٱلۡحَقِّ وَبِهِۦ يَعۡدِلُونَ

Ndipo mwa anthu a Mûsa, mudali gulu lomwe linkatsogolera anzawo ku choonadi. Ndipo ndi choonadicho ankachita chilungamo. info
التفاسير: