Traduzione dei Significati del Sacro Corano - Traduzione chicheŵa - Khalid Ibrahim Betyala

external-link copy
21 : 59

لَوۡ أَنزَلۡنَا هَٰذَا ٱلۡقُرۡءَانَ عَلَىٰ جَبَلٖ لَّرَأَيۡتَهُۥ خَٰشِعٗا مُّتَصَدِّعٗا مِّنۡ خَشۡيَةِ ٱللَّهِۚ وَتِلۡكَ ٱلۡأَمۡثَٰلُ نَضۡرِبُهَا لِلنَّاسِ لَعَلَّهُمۡ يَتَفَكَّرُونَ

Chikhala kuti tidaivumbulutsa Qur’an iyi pamwamba pa phiri, ukadaliona phirilo lili lodzichepetsa ndi kung’ambika chifukwa choopa Allah. Ndipo awa ndi mafanizo omwe tikuwapereka kwa anthu kuti aganizire. info
التفاسير: