Traduction des sens du Noble Coran - La traduction tchétchène - Khâlid Ibrâhîm Bîtâlâ

external-link copy
78 : 4

أَيۡنَمَا تَكُونُواْ يُدۡرِككُّمُ ٱلۡمَوۡتُ وَلَوۡ كُنتُمۡ فِي بُرُوجٖ مُّشَيَّدَةٖۗ وَإِن تُصِبۡهُمۡ حَسَنَةٞ يَقُولُواْ هَٰذِهِۦ مِنۡ عِندِ ٱللَّهِۖ وَإِن تُصِبۡهُمۡ سَيِّئَةٞ يَقُولُواْ هَٰذِهِۦ مِنۡ عِندِكَۚ قُلۡ كُلّٞ مِّنۡ عِندِ ٱللَّهِۖ فَمَالِ هَٰٓؤُلَآءِ ٱلۡقَوۡمِ لَا يَكَادُونَ يَفۡقَهُونَ حَدِيثٗا

Paliponse pamene mungakhale imfa ikupezani ngakhale mutakhala m’malinga olimba, ndipo ngati ubwino utawafika (opembedza mafano ndi achiphamaso) amati: “Ubwinowu, ukuchokera kwa Allah.” Koma choipa chikawafikira, amati: “Ichi chachitika chifukwa cha iwe (Muhammad).” Nena: “Zonse zachokera kwa Allah.” Kodi ngotani anthu awa, sangathe kuzindikira nkhani? info
التفاسير: