Traducción de los significados del Sagrado Corán - Traducción al Chewa - Khaled Ibrahim Betala

external-link copy
40 : 10

وَمِنۡهُم مَّن يُؤۡمِنُ بِهِۦ وَمِنۡهُم مَّن لَّا يُؤۡمِنُ بِهِۦۚ وَرَبُّكَ أَعۡلَمُ بِٱلۡمُفۡسِدِينَ

Ndipo mwa iwo pali ena omwe akuikhulupirira (Qur’an), ndipo ena mwa iwo sakuikhulupirira. Ndipo Mbuye wako akuwadziwa bwino oononga. info
التفاسير: