Translation of the Meanings of the Noble Qur'an - Chewa translation - Khaled Ibrahim Batyala

external-link copy
3 : 98

فِيهَا كُتُبٞ قَيِّمَةٞ

Omwe mkati mwake muli malamulo oongoka (ofotokoza za choona).[468] info

[468] Kapena kuti “mkati mwake muli mabuku olingana,” ndiye kuti m’Qur’an muli zophunzitsa za mabuku onse omwe Allah adavumbulutsa kwa Aneneri onse akale.

التفاسير: