Prijevod značenja časnog Kur'ana - Prijevod na čeva jezik - Halid Ibrahim Betala

external-link copy
9 : 10

إِنَّ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ يَهۡدِيهِمۡ رَبُّهُم بِإِيمَٰنِهِمۡۖ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهِمُ ٱلۡأَنۡهَٰرُ فِي جَنَّٰتِ ٱلنَّعِيمِ

Ndithu amene akhulupirira ndi kumachita zabwino, Mbuye wawo awaongola chifukwa cha chikhulupiliro chawo. Pansi (ndi patsogolo) pawo mitsinje ikuyenda m’Minda yamtendere. info
التفاسير: