పవిత్ర ఖురాన్ యొక్క భావార్థాల అనువాదం - చిచియో అనువాదం - ఖాలిద్ ఇబ్రాహీమ్ బైతాలా

At-Takwîr

external-link copy
1 : 81

إِذَا ٱلشَّمۡسُ كُوِّرَتۡ

Pamene dzuwa lidzakulungidwe (ndikuchotsedwa kuwala kwake),[388] info

[388] Surah zambiri zimene zidavumbulutsidwa ku Makka zimanena zododometsa za tsiku lachimaliziro.

التفاسير: