ಪವಿತ್ರ ಕುರ್‌ಆನ್ ಅರ್ಥಾನುವಾದ - ಚೇವಾ ಅನುವಾದ - ಖಾಲಿದ್ ಇಬ್ರಾಹೀಂ ಬೀತಾಲಾ

Al-Ikhlâs

external-link copy
1 : 112

قُلۡ هُوَ ٱللَّهُ أَحَدٌ

Nena (iwe Mtumiki (s.a.w), kwa amene akukufunsa mwachipongwe, mbiri za Mulungu wako): “Iye ndi Allah Mmodzi, (alibe mnzake). info
التفاسير:

external-link copy
2 : 112

ٱللَّهُ ٱلصَّمَدُ

Allah ndi Wokhala ndi zonse Wodaliridwa ndi zolengedwa Zake. info
التفاسير:

external-link copy
3 : 112

لَمۡ يَلِدۡ وَلَمۡ يُولَدۡ

Sadabale (mwana) ndiponso sadaberekedwe. info
التفاسير:

external-link copy
4 : 112

وَلَمۡ يَكُن لَّهُۥ كُفُوًا أَحَدُۢ

Ndiponso palibe aliyense wofanana ndi Iye.” info
التفاسير: