Terjemahan makna Alquran Alkarim - Terjemahan Berbahasa Chichewa - Khalid Ibrahim Betala

external-link copy
60 : 7

قَالَ ٱلۡمَلَأُ مِن قَوۡمِهِۦٓ إِنَّا لَنَرَىٰكَ فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٖ

Akuluakulu a mwa anthu ake adati: “Ndithu ife tikukuona kuti uli m’kusokera koonekera (potiletsa izi zomwe tidawapeza nazo makolo athu).” info
التفاسير: