કુરઆન મજીદના શબ્દોનું ભાષાંતર - ચિચેવા ભાષામાં અનુવાદ - ખાલિદ ઇબ્રાહિમ બૈતાલા

external-link copy
78 : 6

فَلَمَّا رَءَا ٱلشَّمۡسَ بَازِغَةٗ قَالَ هَٰذَا رَبِّي هَٰذَآ أَكۡبَرُۖ فَلَمَّآ أَفَلَتۡ قَالَ يَٰقَوۡمِ إِنِّي بَرِيٓءٞ مِّمَّا تُشۡرِكُونَ

Pamene adaona dzuwa likutuluka, adati: “Uyu ndiye mbuye wanga; uyu ngwamkulu kwabasi.” Koma pamene lidalowa, adati: “E inu anthu anga! Ine ndili kutali ndi zomwe mukumphatikiza nazo (Allah). info
التفاسير: