કુરઆન મજીદના શબ્દોનું ભાષાંતર - ચિચેવા ભાષામાં અનુવાદ - ખાલિદ ઇબ્રાહિમ બૈતાલા

external-link copy
162 : 6

قُلۡ إِنَّ صَلَاتِي وَنُسُكِي وَمَحۡيَايَ وَمَمَاتِي لِلَّهِ رَبِّ ٱلۡعَٰلَمِينَ

Nena: “Ndithudi, Swala yanga, mapemphero anga onse, moyo wanga, ndi imfa yanga, (zonse) nza Allah, Mbuye wa zolengedwa zonse.” info
التفاسير: