Firo maanaaji al-quraan tedduɗo oo - Eggo e ɗemngal Ciiciiwa - Kaalid Ibrahiima Biitala.

external-link copy
133 : 6

وَرَبُّكَ ٱلۡغَنِيُّ ذُو ٱلرَّحۡمَةِۚ إِن يَشَأۡ يُذۡهِبۡكُمۡ وَيَسۡتَخۡلِفۡ مِنۢ بَعۡدِكُم مَّا يَشَآءُ كَمَآ أَنشَأَكُم مِّن ذُرِّيَّةِ قَوۡمٍ ءَاخَرِينَ

Ndipo Mbuye wako Ngokwanira (Wolemera), Mwini chifundo. Ngati afuna angakuchotseni ndi kuwaika m’malo mwanu amene wawafuna monga momwe adakulengerani kuchokera m’mbumba ya anthu ena. info
التفاسير: