Firo maanaaji al-quraan tedduɗo oo - Eggo e ɗemngal Ciiciiwa - Kaalid Ibrahiima Biitala.

external-link copy
132 : 6

وَلِكُلّٖ دَرَجَٰتٞ مِّمَّا عَمِلُواْۚ وَمَا رَبُّكَ بِغَٰفِلٍ عَمَّا يَعۡمَلُونَ

Ndipo onse adzakhala ndi nyota (za ulemelero) kuchokera m’zochita zawo. Ndipo Mbuye wako sali wamphwayi pa zimene akuchita. info
التفاسير: