ترجمهٔ معانی قرآن کریم - ترجمه‌ى چوایی - خالد ابراهیم بيتالا

external-link copy
15 : 81

فَلَآ أُقۡسِمُ بِٱلۡخُنَّسِ

Ndikulumbilira nyenyezi zimene zimabwerera masana ndi kutulukanso usiku. info
التفاسير: